Deuteronomo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa muzimupatula nʼkumupereka kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwiritse ntchito iliyonse mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe,* kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.
19 Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa muzimupatula nʼkumupereka kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwiritse ntchito iliyonse mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe,* kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.