Deuteronomo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chaka chilichonse inuyo ndi banja lanu muzidzadya mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene Yehova adzasankhe.+
20 Chaka chilichonse inuyo ndi banja lanu muzidzadya mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene Yehova adzasankhe.+