Deuteronomo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Muziidyera mumzinda wanu* ngati mmene mumadyera insa ndi mbawala.+ Munthu wodetsedwa komanso munthu woyera nayenso azidya nawo.
22 Muziidyera mumzinda wanu* ngati mmene mumadyera insa ndi mbawala.+ Munthu wodetsedwa komanso munthu woyera nayenso azidya nawo.