Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2136, 2244
16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+