Deuteronomo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamapezeke ndi mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa mʼdziko lanu lonse kwa masiku 7.+ Nyama iliyonse imene mwapereka nsembe madzulo, pa tsiku loyamba, isamagone mpaka mʼmawa.+
4 Musamapezeke ndi mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa mʼdziko lanu lonse kwa masiku 7.+ Nyama iliyonse imene mwapereka nsembe madzulo, pa tsiku loyamba, isamagone mpaka mʼmawa.+