Deuteronomo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma muzidzapereka nsembe ya Pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuikapo dzina lake. Muzidzapereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene munatuluka mu Iguputo. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:6 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, ptsa. 13-14
6 Koma muzidzapereka nsembe ya Pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuikapo dzina lake. Muzidzapereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene munatuluka mu Iguputo.