Deuteronomo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzidya mkate wopanda zofufumitsa kwa masiku 6, ndipo pa tsiku la 7 muzichitira Yehova Mulungu wanu msonkhano wapadera. Pa tsikuli musamagwire ntchito.+
8 Muzidya mkate wopanda zofufumitsa kwa masiku 6, ndipo pa tsiku la 7 muzichitira Yehova Mulungu wanu msonkhano wapadera. Pa tsikuli musamagwire ntchito.+