Deuteronomo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muzichita Chikondwerero cha Misasa+ kwa masiku 7, mukamatuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.
13 Muzichita Chikondwerero cha Misasa+ kwa masiku 7, mukamatuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.