Deuteronomo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ inuyo, mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, Mlevi, mlendo amene akukhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.
14 Muzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ inuyo, mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, Mlevi, mlendo amene akukhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.