Deuteronomo 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso imene aliyense ayenera kubweretsa izikhala yogwirizana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 46 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 196-197
17 Mphatso imene aliyense ayenera kubweretsa izikhala yogwirizana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+