Deuteronomo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musamakhotetse chilungamo,+ musamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ komanso kupotoza mawu a anthu olungama. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:19 Nsanja ya Olonda,2/15/1989, tsa. 12
19 Musamakhotetse chilungamo,+ musamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ komanso kupotoza mawu a anthu olungama.