Deuteronomo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzichita zinthu mwachilungamo+ kuti mukhale ndi moyo nʼkukatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.
20 Muzichita zinthu mwachilungamo+ kuti mukhale ndi moyo nʼkukatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.