Deuteronomo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musadzadzale mtengo uliwonse kuti ukhale mzati wopatulika*+ pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wanu limene mudzapange.
21 Musadzadzale mtengo uliwonse kuti ukhale mzati wopatulika*+ pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wanu limene mudzapange.