Deuteronomo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 moti wasochera ndipo amalambira milungu ina nʼkumaigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena gulu lonse la zinthu zakuthambo,+ zomwe ine sindinakulamuleni,+
3 moti wasochera ndipo amalambira milungu ina nʼkumaigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena gulu lonse la zinthu zakuthambo,+ zomwe ine sindinakulamuleni,+