Deuteronomo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene adzachite zinthu modzikuza posamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wanu kapena woweruza, ayenera kufa.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+
12 Munthu amene adzachite zinthu modzikuza posamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wanu kapena woweruza, ayenera kufa.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+