Deuteronomo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 angathe kumatumikira kumeneko mʼdzina la Yehova Mulungu wake mofanana ndi Alevi onse, omwe ndi abale ake, amene akutumikira kumeneko pamaso pa Yehova.+
7 angathe kumatumikira kumeneko mʼdzina la Yehova Mulungu wake mofanana ndi Alevi onse, omwe ndi abale ake, amene akutumikira kumeneko pamaso pa Yehova.+