Deuteronomo 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzakupatsani mneneriyu poyankha zimene munapempha Yehova Mulungu wanu ku Horebe, tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Paja munapempha kuti, ‘Mutilole kuti tisamvenso mawu a Yehova Mulungu wathu kapena kuona moto waukuluwu, kuopera kuti tingafe.’+
16 Adzakupatsani mneneriyu poyankha zimene munapempha Yehova Mulungu wanu ku Horebe, tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Paja munapempha kuti, ‘Mutilole kuti tisamvenso mawu a Yehova Mulungu wathu kapena kuona moto waukuluwu, kuopera kuti tingafe.’+