-
Deuteronomo 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mneneri akalankhula mʼdzina la Yehova, koma zimene walankhulazo osachitika kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo. Mneneriyo walankhula mawu amenewo modzikuza ndipo musachite naye mantha.’”
-