Deuteronomo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Yehova Mulungu wanu akadzawononga mitundu yamʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, inu nʼkuwalandadi dzikolo ndi kukhala mʼmizinda yawo komanso mʼnyumba zawo,+
19 “Yehova Mulungu wanu akadzawononga mitundu yamʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, inu nʼkuwalandadi dzikolo ndi kukhala mʼmizinda yawo komanso mʼnyumba zawo,+