Deuteronomo 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mudzapatule mizinda itatu pakati pa dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu.+
2 mudzapatule mizinda itatu pakati pa dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu.+