-
Deuteronomo 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mudzagawe mʼzigawo zitatu dziko limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani kuti likhale lanu, ndipo mudzalambule misewu yopita kumizindayo kuti aliyense wopha munthu azithawira kumizinda imeneyo.
-