Deuteronomo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiye zimene zizichitika ndi munthu amene wapha mnzake nʼkuthawira kumeneko kuti akhale ndi moyo ndi izi: Ngati wapha mnzake mwangozi ndipo sankadana naye,+
4 Ndiye zimene zizichitika ndi munthu amene wapha mnzake nʼkuthawira kumeneko kuti akhale ndi moyo ndi izi: Ngati wapha mnzake mwangozi ndipo sankadana naye,+