5 mwachitsanzo, munthu akapita ndi mnzake kuthengo kukafuna nkhuni, ndipo wakweza dzanja lake kuti adule mtengo ndi nkhwangwa koma nkhwangwayo yaguluka mumpini wake nʼkumenya mnzakeyo mpaka kumupha, amene wapha mnzakeyo azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi kuti akhale ndi moyo.+