Deuteronomo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (ngati mutatsatira mokhulupirika malamulo onsewa amene ndikukupatsani lero, akuti muzikonda Yehova Mulungu wanu komanso kuyenda mʼnjira zake nthawi zonse+) mudzawonjezere mizinda inanso itatu pa mizinda imeneyi.+
9 (ngati mutatsatira mokhulupirika malamulo onsewa amene ndikukupatsani lero, akuti muzikonda Yehova Mulungu wanu komanso kuyenda mʼnjira zake nthawi zonse+) mudzawonjezere mizinda inanso itatu pa mizinda imeneyi.+