Deuteronomo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukamachita zimenezi simudzakhetsa magazi a munthu wosalakwa+ mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ngati cholowa ndipo simudzakhala ndi mlandu wa magazi.+
10 Mukamachita zimenezi simudzakhetsa magazi a munthu wosalakwa+ mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ngati cholowa ndipo simudzakhala ndi mlandu wa magazi.+