Deuteronomo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musamamumvere* chisoni ndipo muzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendereni bwino.
13 Musamamumvere* chisoni ndipo muzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendereni bwino.