Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musamamve* chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.”+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:21 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yandikirani, ptsa. 131-133
21 Musamamve* chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.”+