-
Deuteronomo 20:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atsogoleri nawonso aziuza anthuwo kuti, ‘Kodi pali amene wamanga nyumba yatsopano koma sanaitsegulire? Achoke nʼkubwerera kunyumba yakeyo, kuopera kuti angafe pankhondo, ndipo munthu wina angatsegulire nyumbayo.
-