Deuteronomo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi pali amene analonjeza mkazi kuti adzamukwatira koma sanamukwatire? Achoke nʼkubwerera kunyumba yake,+ kuopera kuti angafe pankhondo ndipo mwamuna wina angakwatire mkaziyo.’
7 Kodi pali amene analonjeza mkazi kuti adzamukwatira koma sanamukwatire? Achoke nʼkubwerera kunyumba yake,+ kuopera kuti angafe pankhondo ndipo mwamuna wina angakwatire mkaziyo.’