Deuteronomo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atsogoleriwo afunsenso anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha komanso wosalimba mtima?+ Abwerere kunyumba yake, kuti asachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene iye wachitira.’*+
8 Atsogoleriwo afunsenso anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha komanso wosalimba mtima?+ Abwerere kunyumba yake, kuti asachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene iye wachitira.’*+