Deuteronomo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati anthu amumzindawo akuyankhani mwamtendere nʼkukutsegulirani mageti ake, anthu onse opezeka mmenemo azikhala anu kuti azikugwirirani ntchito yaukapolo ndipo azikutumikirani.+
11 Ngati anthu amumzindawo akuyankhani mwamtendere nʼkukutsegulirani mageti ake, anthu onse opezeka mmenemo azikhala anu kuti azikugwirirani ntchito yaukapolo ndipo azikutumikirani.+