Deuteronomo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma muzitenga akazi, ana aangʼono, ziweto ndi chilichonse chopezeka mumzindawo kuti zikhale zanu,+ ndipo muzidya zimene mwatenga kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
14 Koma muzitenga akazi, ana aangʼono, ziweto ndi chilichonse chopezeka mumzindawo kuti zikhale zanu,+ ndipo muzidya zimene mwatenga kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+