Deuteronomo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mʼmizinda ya anthu awa, imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, musalole kuti mutsale chamoyo chilichonse.+
16 Koma mʼmizinda ya anthu awa, imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, musalole kuti mutsale chamoyo chilichonse.+