Deuteronomo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmalomwake, mudzawononge anthu onse. Mudzawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani.
17 Mʼmalomwake, mudzawononge anthu onse. Mudzawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani.