Deuteronomo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukawawononge kuti asakakuphunzitseni kuchita zinthu zonse zonyansa zimene achitira milungu yawo nʼkukuchititsani kuti muchimwire Yehova Mulungu wanu.+
18 Mukawawononge kuti asakakuphunzitseni kuchita zinthu zonse zonyansa zimene achitira milungu yawo nʼkukuchititsani kuti muchimwire Yehova Mulungu wanu.+