-
Deuteronomo 20:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mungathe kuwononga mtengo wokhawo umene mukuudziwa kuti subereka zipatso zakudya. Mtengo woterowo mungaudule nʼkumangira mpanda wozungulira mzinda wa adani amene akuchita nanu nkhondo, mpaka mzindawo utagwa.”
-