-
Deuteronomo 21:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno akulu amumzinda umene uli pafupi ndi pamene papezeka munthu wakufayo, azitenga ngʼombe yaingʼono yaikazi imene sanaigwiritsepo ntchito, imene sinasenzepo goli nʼkukoka chilichonse.
-