-
Deuteronomo 21:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mukadzachita zimenezi mudzachotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa pakati panu, chifukwa mudzakhala mutachita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova.
-