13 Azisintha zovala zimene anavala pa nthawi imene ankagwidwa ukapolo ndipo azikhala mʼnyumba mwanu. Azilira maliro a bambo ake ndi a mayi ake kwa mwezi wathunthu,+ kenako mungathe kugona naye. Inu mudzakhala mwamuna wake ndipo iye adzakhala mkazi wanu.