17 Azivomereza kuti mwana wamwamuna wa mkazi wake wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa, pomupatsa magawo awiri pa chilichonse chimene ali nacho chifukwa iye ndi chiyambi cha mphamvu zake zobereka. Mwana ameneyo ndi amene ali woyenera kulandira udindo wa mwana woyamba kubadwa.+