Deuteronomo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+
18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+