Deuteronomo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mukaona ngʼombe kapena nkhosa ya mʼbale wanu ikusochera, musamangoisiya osaibweza.+ Muziikusa nʼkuipititsa kwa mʼbale wanuyo.
22 “Mukaona ngʼombe kapena nkhosa ya mʼbale wanu ikusochera, musamangoisiya osaibweza.+ Muziikusa nʼkuipititsa kwa mʼbale wanuyo.