Deuteronomo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma ngati mwiniwake sakhala pafupi ndi inu kapena simukumudziwa, muzitenga chiwetocho nʼkupita nacho kunyumba kwanu. Muzisunga chiwetocho mpaka mwiniwakeyo atafika kudzachifufuza ndipo muzimubwezera.+
2 Koma ngati mwiniwake sakhala pafupi ndi inu kapena simukumudziwa, muzitenga chiwetocho nʼkupita nacho kunyumba kwanu. Muzisunga chiwetocho mpaka mwiniwakeyo atafika kudzachifufuza ndipo muzimubwezera.+