-
Deuteronomo 22:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Muzichita zimenezi ndi bulu wa mʼbale wanu, nsalu yake, kapena chilichonse chimene mʼbale wanu wataya inu nʼkuchipeza. Simukuyenera kungochisiya osachitola.
-