-
Deuteronomo 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mkazi asamavale chovala cha mwamuna ndipo mwamuna asamavale chovala cha mkazi. Chifukwa aliyense wochita zimenezi ndi wonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.
-