Deuteronomo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bambo a mtsikanayo aziuza akuluwo kuti, ‘Ine ndinapereka mwana wanga wamkazi kwa mwamuna uyu kuti akhale mkazi wake koma akudana naye,*
16 Bambo a mtsikanayo aziuza akuluwo kuti, ‘Ine ndinapereka mwana wanga wamkazi kwa mwamuna uyu kuti akhale mkazi wake koma akudana naye,*