Deuteronomo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 onse awiri muziwapititsa kugeti la mzindawo nʼkuwaponya miyala kuti afe. Mtsikanayo afe chifukwa chakuti sanakuwe mumzindawo ndipo mwamunayo afe chifukwa waipitsa mkazi wa mnzake.+ Choncho muzichotsa oipawo pakati panu. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, tsa. 14
24 onse awiri muziwapititsa kugeti la mzindawo nʼkuwaponya miyala kuti afe. Mtsikanayo afe chifukwa chakuti sanakuwe mumzindawo ndipo mwamunayo afe chifukwa waipitsa mkazi wa mnzake.+ Choncho muzichotsa oipawo pakati panu.