Deuteronomo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtsikanayo musamuchite chilichonse. Iye sanachite tchimo loyenera imfa. Mlanduwu ukufanana ndi wa munthu amene waukira mnzake nʼkumupha.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2019, tsa. 14
26 Mtsikanayo musamuchite chilichonse. Iye sanachite tchimo loyenera imfa. Mlanduwu ukufanana ndi wa munthu amene waukira mnzake nʼkumupha.+