Deuteronomo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo, ndipo azikhala mkazi wake.+ Chifukwa chakuti wamuchititsa manyazi, sadzaloledwa kumusiya masiku onse a moyo wake. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:29 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 31
29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo, ndipo azikhala mkazi wake.+ Chifukwa chakuti wamuchititsa manyazi, sadzaloledwa kumusiya masiku onse a moyo wake.