Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+
7 Musamadane ndi mbadwa ya Edomu, chifukwa ndi mʼbale wanu.+ Musamadane ndi munthu wa ku Iguputo, chifukwa munali alendo mʼdziko lawo.+